Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Ukakwatira mkazi, usavule mwana wake wamkazi.+ Usatenge mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wa mkazi wakoyo kuti um’vule. Usatengenso mwana wamkazi wa mwana wake wamkazi kuti um’vule. Limeneli ndi khalidwe lotayirira+ chifukwa amenewa ndi achibale.

  • Deuteronomo 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Usabweretse malipiro+ a hule kapena malipiro a galu*+ m’nyumba ya Yehova Mulungu wako kuti ukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa zonsezo ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.

  • Oweruza 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+

  • 1 Samueli 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ndinaganiza+ kuti, ‘Tsopano Afilisitiwa abwera ku Giligala kuno kudzamenyana nane, ndipo sindinakhazike pansi mtima wa Yehova kuti atikomere mtima.’ Choncho ndakakamizika+ kupereka nsembe yopsereza.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena