Levitiko 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu. Deuteronomo 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Wotembereredwa ndi mwamuna wogona ndi apongozi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
14 “‘Mwamuna akakwatira mkazi n’kugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lotayirira.+ Aziphedwa ndi kutenthedwa,+ onse mwamunayo ndi akaziwo, kuti khalidwe lotayirira+ lisapitirire pakati panu.
23 “‘Wotembereredwa ndi mwamuna wogona ndi apongozi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)