Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma anthu ali m’tulo, kunabwera mdani wake. Mdaniyo anafesa namsongole m’munda wa tiriguwo, n’kuchoka.

  • Mateyu 13:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Munda ndiwo dziko+ ndipo mbewu zabwino ndi ana a ufumu. Koma namsongole ndi ana a woipayo,+

  • Agalatiya 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chifukwa cha abale onyenga+ amene analowa pakati pathu mwakachetechete+ ndiponso mozemba monga akazitape, n’cholinga choti awononge ufulu wathu+ umene tili nawo mogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso kuti atisandutse akapolo+ . . .

  • 1 Yohane 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena