Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tamva kuti ena ochokera pakati pathu akhala akulankhula mawu okusautsani,+ pofuna kupotoza maganizo anu, ngakhale kuti ife sitinawapatse malangizo aliwonse.+

  • 2 Akorinto 11:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pa maulendo kawirikawiri, zoopsa za m’mitsinje, zoopsa za achifwamba pamsewu,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mtundu wanga,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mitundu ina,+ zoopsa mumzinda,+ zoopsa m’chipululu, zoopsa za panyanja, zoopsa pakati pa abale onyenga,

  • Yuda 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndatero chifukwa chakuti anthu ena alowa mozemba pakati pathu.+ Anthu amenewa Malemba anawasonyezeratu kalekale+ kuti adzaweruzidwa.+ Iwo ndiwo anthu osaopa Mulungu+ amene atenga kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu kukhala chifukwa chochitira khalidwe lotayirira,+ ndipo akhala osakhulupirika+ kwa Ambuye wathu mmodzi yekha+ amene anatigula,+ Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena