Agalatiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha abale onyenga+ amene analowa pakati pathu mwakachetechete+ ndiponso mozemba monga akazitape, n’cholinga choti awononge ufulu wathu+ umene tili nawo mogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso kuti atisandutse akapolo+ . . . Tito 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa.
4 Chifukwa cha abale onyenga+ amene analowa pakati pathu mwakachetechete+ ndiponso mozemba monga akazitape, n’cholinga choti awononge ufulu wathu+ umene tili nawo mogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso kuti atisandutse akapolo+ . . .
10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa.