Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Yohane 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho ngati Mwana wakumasulani, mudzakhaladi omasuka.+ 2 Akorinto 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Yehova ndiye Mzimu,+ ndipo pamene pali mzimu+ wa Yehova,+ pali ufulu.+ Agalatiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+ 1 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani mfulu,+ koma ufulu wanu usakhale ngati chophimbira zoipa,+ koma monga akapolo a Mulungu.+
5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+