1 Akorinto 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khalani maso,+ limbani m’chikhulupiriro,+ pitirizani kuchita chamuna,+ khalani amphamvu.+ Afilipi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho abale anga okondedwa, inu amene ndimakukondani ndiponso amene ndimalakalaka kukuonani, inu chimwemwe changa ndi chisoti changa chaulemerero,+ pitirizani kulimbikira+ mwa Ambuye.
4 Choncho abale anga okondedwa, inu amene ndimakukondani ndiponso amene ndimalakalaka kukuonani, inu chimwemwe changa ndi chisoti changa chaulemerero,+ pitirizani kulimbikira+ mwa Ambuye.