Agalatiya 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso ngati mukutsogoleredwa ndi mzimu,+ simuli pansi pa chilamulo.+