Genesis 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake, Yehova anati: “Mzimu wanga+ supitiriza mpaka kalekale kulezera mtima anthu,+ popeza alinso athupi.+ Choncho, masiku a moyo wawo adzangokhala zaka 120.”+ Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
3 Pambuyo pake, Yehova anati: “Mzimu wanga+ supitiriza mpaka kalekale kulezera mtima anthu,+ popeza alinso athupi.+ Choncho, masiku a moyo wawo adzangokhala zaka 120.”+
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+