Aroma 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Bwanji ngati Mulungu analekerera moleza mtima kwambiri ziwiya za mkwiyo zoyenera kuwonongedwa ngakhale kuti akufuna kuonetsa mkwiyo wake ndi mphamvu zake?+ 1 Petulo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 imene inali yosamvera+ pa nthawi imene Mulungu anali kuleza mtima+ m’masiku a Nowa, pamene chingalawa chinali kupangidwa,+ chimene chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, miyoyo 8 yokha.+ 2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+
22 Bwanji ngati Mulungu analekerera moleza mtima kwambiri ziwiya za mkwiyo zoyenera kuwonongedwa ngakhale kuti akufuna kuonetsa mkwiyo wake ndi mphamvu zake?+
20 imene inali yosamvera+ pa nthawi imene Mulungu anali kuleza mtima+ m’masiku a Nowa, pamene chingalawa chinali kupangidwa,+ chimene chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, miyoyo 8 yokha.+
9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+