Aroma 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+ Aroma 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!” Agalatiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+ Agalatiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+
14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+
15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!”
5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+
13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+