Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Aroma 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inde, popeza munamasulidwa+ ku uchimo, munakhala akapolo+ a chilungamo.+