Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Agalatiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+
5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu.+ Chotero khalani olimba,+ ndipo musalole kumangidwanso m’goli laukapolo.+