2 Akorinto 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo mumalolera aliyense wokumangani ukapolo,+ womeza zimene muli nazo, wokulandani zimene muli nazo, wodzikweza pa inu, ndiponso aliyense wokuwombani mbama.+ Agalatiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+
20 Ndipo mumalolera aliyense wokumangani ukapolo,+ womeza zimene muli nazo, wokulandani zimene muli nazo, wodzikweza pa inu, ndiponso aliyense wokuwombani mbama.+
9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+