Mateyu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+ Mateyu 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ine ndidzawauza momveka bwino kuti: Sindikukudziwani ngakhale pang’ono!+ Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.+ Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+ 2 Atesalonika 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zoona, chinsinsi cha kusamvera malamulo kumeneku chilipo kale,+ koma chingokhalapo kufikira atachoka amene panopa ali choletsa.+
15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+
23 Koma ine ndidzawauza momveka bwino kuti: Sindikukudziwani ngakhale pang’ono!+ Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.+
24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+
7 Zoona, chinsinsi cha kusamvera malamulo kumeneku chilipo kale,+ koma chingokhalapo kufikira atachoka amene panopa ali choletsa.+