Luka 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwininyumba akanyamuka ndi kukakhoma chitseko, ndiyeno inu n’kuima panja ndi kuyamba kugogoda pachitsekopo, n’kumanena kuti, ‘Titsegulireni ambuye,’+ iye poyankha adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’+
25 Mwininyumba akanyamuka ndi kukakhoma chitseko, ndiyeno inu n’kuima panja ndi kuyamba kugogoda pachitsekopo, n’kumanena kuti, ‘Titsegulireni ambuye,’+ iye poyankha adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’+