Mateyu 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pambuyo pake anamwali ena aja nawonso anafika n’kunena kuti, ‘Ambuye, ambuye, titsegulireni!’+ Luka 6:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Nanga n’chifukwa chiyani mumandiitana kuti ‘Ambuye! Ambuye!’ koma osachita zimene ndimanena?+