Luka 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwininyumba akanyamuka ndi kukakhoma chitseko, ndiyeno inu n’kuima panja ndi kuyamba kugogoda pachitsekopo, n’kumanena kuti, ‘Titsegulireni ambuye,’+ iye poyankha adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’+ Aheberi 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, atafunanso kulandira dalitso monga cholowa chake,+ anamukanira.+ Pakuti ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse, kwinaku akugwetsa misozi,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.+
25 Mwininyumba akanyamuka ndi kukakhoma chitseko, ndiyeno inu n’kuima panja ndi kuyamba kugogoda pachitsekopo, n’kumanena kuti, ‘Titsegulireni ambuye,’+ iye poyankha adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera.’+
17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, atafunanso kulandira dalitso monga cholowa chake,+ anamukanira.+ Pakuti ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse, kwinaku akugwetsa misozi,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.+