Salimo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+ Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+
6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+