Salimo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+ Luka 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma iye adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera. Ndichokereni pano, nonsenu ochita zinthu zosalungama!’+ 1 Yohane 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense amene amachita tchimo+ samvera malamulo,+ choncho tchimo+ ndilo kusamvera malamulo.
8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+
27 Koma iye adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera. Ndichokereni pano, nonsenu ochita zinthu zosalungama!’+