Salimo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse amene mumachita zoipa,Chifukwa Yehova adzamva mawu a kulira kwanga.+
8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse amene mumachita zoipa,Chifukwa Yehova adzamva mawu a kulira kwanga.+