Salimo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+
8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+