Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Munthu aliyense akamva mawu a ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera n’kukwatula zomwe zafesedwa mumtima wa munthuyo. Izi ndi zofesedwa m’mbali mwa msewu zija.

  • Luka 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Mdyerekezi anamuuza kuti: “Ndikupatsani ulamuliro+ pa maufumu onsewa ndi ulemerero wawo wonse, chifukwa unaperekedwa kwa ine. Ndikhoza kuupereka kwa aliyense amene ndakonda kum’patsa.+

  • Yohane 12:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+

  • Aheberi 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero, popeza kuti “ana” amenewo onse ndi amagazi ndi mnofu, iyenso anakhala wamagazi ndi mnofu.+ Anachita izi kuti kudzera mu imfa yake,+ awononge+ Mdyerekezi,+ amene ali ndi njira yobweretsera imfa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena