Yohane 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+ Yohane 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sindilankhula nanunso zambiri, pakuti wolamulira+ wa dziko akubwera. Iye alibe mphamvu pa ine,+ Aefeso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+
2 Munali kuyenda m’zimenezo mogwirizana ndi nthawi*+ za m’dzikoli, momveranso wolamulira+ wa mpweya umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe kameneka,+ tsopano kakugwira ntchito mwa ana a kusamvera.+