Maliko 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero anthu amenewa, ndiwo mbewu zimene zimagwera m’mphepete mwa msewu kumene mawu afesedwa. Koma atangomva mawuwo, Satana amabwera+ ndi kuchotsa mawu ofesedwa mwa iwo.+ Luka 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zogwera m’mbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo.+ Kenako Mdyerekezi+ amabwera ndi kudzachotsa mawuwo m’mitima yawo kuti asakhulupirire ndi kupulumuka.+ 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+
15 Chotero anthu amenewa, ndiwo mbewu zimene zimagwera m’mphepete mwa msewu kumene mawu afesedwa. Koma atangomva mawuwo, Satana amabwera+ ndi kuchotsa mawu ofesedwa mwa iwo.+
12 Zogwera m’mbali mwa msewuzo ndi anthu amene amamva mawuwo.+ Kenako Mdyerekezi+ amabwera ndi kudzachotsa mawuwo m’mitima yawo kuti asakhulupirire ndi kupulumuka.+
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+