2 Akorinto 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuti Satana asatichenjerere,+ pakuti tikudziwa bwino ziwembu zake.+