Deuteronomo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+ Yoswa 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa umu ndi mmene Yehova azichitira ndi adani anu onse amene mukumenyana nawo.”+
8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+
25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa umu ndi mmene Yehova azichitira ndi adani anu onse amene mukumenyana nawo.”+