Yesaya 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Anthu inu mukabwerera kwa ine n’kusiya zimene mukuchita, mudzapulumuka. Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”+ Koma inu simunafune.+ Maliro 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndi bwino kuti munthu ayembekezere+ chipulumutso cha Yehova+ moleza mtima.+
15 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Anthu inu mukabwerera kwa ine n’kusiya zimene mukuchita, mudzapulumuka. Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”+ Koma inu simunafune.+