Salimo 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+ Salimo 116:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amateteza anthu osadziwa zambiri.+Ndinali wosautsika koma iye anandipulumutsa.+ Miyambo 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usanene kuti: “Ndidzabwezera choipa.”+ Khulupirira Yehova+ ndipo iye adzakupulumutsa.+
6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+