1 Mbiri 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+ 2 Mbiri 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi Aitiyopiya+ ndi Alibiya+ sanali gulu lankhondo lalikulu, la anthu ambiri, magaleta ambiri, ndi okwera pamahatchi ambirinso?+ Chifukwa chakuti munadalira Yehova, kodi iye sanawapereke m’manja mwanu?+ Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+
20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+
8 Kodi Aitiyopiya+ ndi Alibiya+ sanali gulu lankhondo lalikulu, la anthu ambiri, magaleta ambiri, ndi okwera pamahatchi ambirinso?+ Chifukwa chakuti munadalira Yehova, kodi iye sanawapereke m’manja mwanu?+
3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+