Yeremiya 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘M’masiku anu ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi m’malo ano, inu mukuona.’+ Habakuku 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+
9 “Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘M’masiku anu ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi m’malo ano, inu mukuona.’+
5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+