Genesis 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Motero, kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse za mmenemo zinamalizidwa kulengedwa.+ Salimo 148:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mutamandeni, inu angelo ake onse.+Mutamandeni, inu khamu lake lonse.+ Mateyu 26:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+
53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+