Salimo 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munaidalitsa ndi kuipatsa zinthu zabwino,+Ndipo pamutu pake munaika chisoti chachifumu chagolide woyengeka bwino.+ Chivumbulutso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nditayang’ana, ndinaona hatchi* yoyera.+ Wokwerapo+ wake ananyamula uta.+ Iye anapatsidwa chisoti chachifumu,+ ndi kupita kukagonjetsa adani ake+ ndipo anapambana pa nkhondo yolimbana nawo.+
3 Munaidalitsa ndi kuipatsa zinthu zabwino,+Ndipo pamutu pake munaika chisoti chachifumu chagolide woyengeka bwino.+
2 Nditayang’ana, ndinaona hatchi* yoyera.+ Wokwerapo+ wake ananyamula uta.+ Iye anapatsidwa chisoti chachifumu,+ ndi kupita kukagonjetsa adani ake+ ndipo anapambana pa nkhondo yolimbana nawo.+