Yobu 39:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Lipenga likangolira, imati eyaa!Imanunkhiza nkhondo ili kutali,Imamva phokoso la mafumu ndi mfuu yankhondo.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+
25 Lipenga likangolira, imati eyaa!Imanunkhiza nkhondo ili kutali,Imamva phokoso la mafumu ndi mfuu yankhondo.+
11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+