Chivumbulutso 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo adzayenda n’kufalikira mpaka kumbali zonse za dziko lapansi, kenako adzazungulira msasa wa oyera,+ ndi mzinda wokondedwa.+ Koma moto udzatsika kuchokera kumwamba ndi kuwapsereza.+
9 Iwo adzayenda n’kufalikira mpaka kumbali zonse za dziko lapansi, kenako adzazungulira msasa wa oyera,+ ndi mzinda wokondedwa.+ Koma moto udzatsika kuchokera kumwamba ndi kuwapsereza.+