Ezekieli 48:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Kuzungulira mzindawo pakhale mtunda wokwana mikono 18,000. Kuyambira pa tsiku limenelo, dzina la mzindawo lidzakhala lakuti, Yehova Ali Kumeneko.”+ Chivumbulutso 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+
35 “Kuzungulira mzindawo pakhale mtunda wokwana mikono 18,000. Kuyambira pa tsiku limenelo, dzina la mzindawo lidzakhala lakuti, Yehova Ali Kumeneko.”+
3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+