Yeremiya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa nthawiyo mzinda wa Yerusalemu adzautcha kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsira+ ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso mitima yawo yoipayo.”+ Yoweli 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Magazi awo amene anali ndi mlandu adzakhala opanda mlandu,+ ndipo Yehova azidzakhala mu Ziyoni.”+ Zekariya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.
17 Pa nthawiyo mzinda wa Yerusalemu adzautcha kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsira+ ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso mitima yawo yoipayo.”+
10 “Fuula kwambiri ndi kusangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,+ pakuti ine ndikubwera+ ndipo ndidzakhala mwa iwe,”+ watero Yehova.