Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 87:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iwe mzinda wa Mulungu woona, anthu akunena za ulemerero wako.+ [Seʹlah.]

  • Yeremiya 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+

  • Ezekieli 43:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo Mulungu anandiuza kuti:

      “Iwe mwana wa munthu, malo awa ndi malo a mpando wanga wachifumu+ ndiponso poikapo mapazi anga.+ Ndidzakhala pamalo amenewa, pakati pa ana a Isiraeli mpaka kalekale.+ A nyumba ya Isiraeli ndi mafumu awo+ sadzaipitsanso dzina langa loyera+ ndi dama lawo komanso ndi mitembo+ ya mafumu awo.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena