Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 47:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mulungu wakhala mfumu ya mitundu ya anthu.+

      Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika.+

  • Yesaya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+

  • Yeremiya 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa nthawiyo mzinda wa Yerusalemu adzautcha kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsira+ ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso mitima yawo yoipayo.”+

  • Ezekieli 1:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamwamba pa thambo limene linali pamwamba pa mitu yawo, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro,+ chooneka ngati mpando wachifumu.+ Pachinthu chooneka ngati mpando wachifumucho, panali winawake wooneka ngati munthu,+ atakhala pamwamba pake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena