Yesaya 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, ife tayembekezera inu pofunafuna njira yanu ya chilungamo.+ Mtima wathu wakhala ukulakalaka kuti ukumbukire dzina lanu, ndi zimene dzinalo limaimira.+ Yesaya 56:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Alendo amene adziphatika kwa Yehova kuti am’tumikire+ ndiponso amene amakonda dzina la Yehova+ n’cholinga choti akhale atumiki ake, onse amene amasunga sabata kuti asalidetse ndiponso amene amatsatira pangano langa,+ Zekariya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’
8 Inu Yehova, ife tayembekezera inu pofunafuna njira yanu ya chilungamo.+ Mtima wathu wakhala ukulakalaka kuti ukumbukire dzina lanu, ndi zimene dzinalo limaimira.+
6 “Alendo amene adziphatika kwa Yehova kuti am’tumikire+ ndiponso amene amakonda dzina la Yehova+ n’cholinga choti akhale atumiki ake, onse amene amasunga sabata kuti asalidetse ndiponso amene amatsatira pangano langa,+
22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’