Zekariya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu idzabwera kudzafunafuna Yehova wa magulu ankhondo akumwamba mu Yerusalemu,+ ndiponso kudzapempha Yehova kuti awakomere mtima.’* Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:22 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 21-22
22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu idzabwera kudzafunafuna Yehova wa magulu ankhondo akumwamba mu Yerusalemu,+ ndiponso kudzapempha Yehova kuti awakomere mtima.’*