Zekariya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:22 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 21-22
22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’