Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake panali chinthu chooneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, choyera ngati kumwamba.+

  • Salimo 96:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake.+

      Mphamvu ndi kukongola zili m’nyumba yake yopatulika.+

  • Ezekieli 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndinapitiriza kuona masomphenya, ndipo ndinaona kuti pamwamba pa thambo+ limene linali pamwamba pa mitu ya akerubi, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro.+ Chinthucho chinalinso chooneka ngati mpando wachifumu,+ ndipo chinali kuonekera pamwamba pa mitu yawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena