Ezekieli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamwamba pa mitu ya zamoyozo, panali chinachake chooneka ngati thambo,+ chonyezimira ngati madzi oundana ochititsa chidwi, choyalidwa pamwamba pa mitu yawo.+
22 Pamwamba pa mitu ya zamoyozo, panali chinachake chooneka ngati thambo,+ chonyezimira ngati madzi oundana ochititsa chidwi, choyalidwa pamwamba pa mitu yawo.+