2 Kenako Davide mfumu anaimirira ndipo anati:
“Ndimvereni inu abale anga ndi anthu anga. Ineyo ndinafunitsitsa mumtima mwanga+ kumanga nyumba yoti likasa la pangano la Yehova lizikhalamo, ndiponso yoti ikhale monga chopondapo mapazi+ cha Mulungu wathu, ndipo ndinakonzekera kuimanga.+