1 Mafumu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Salimo 132:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+
17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+