Salimo 132:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tiyeni tilowe m’chihema chake chachikulu.+Tiyeni tiwerame pachopondapo mapazi ake.+