1 Mbiri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Davide mfumu anaimirira ndipo anati: “Ndimvereni inu abale anga ndi anthu anga. Ineyo ndinafunitsitsa mumtima mwanga+ kumanga nyumba yoti likasa la pangano la Yehova lizikhalamo, ndiponso yoti ikhale monga chopondapo mapazi+ cha Mulungu wathu, ndipo ndinakonzekera kuimanga.+ Salimo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+ Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Salimo 99:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo muweramireni pachopondapo mapazi ake.+Iye ndi woyera.+ Maliro 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.
2 Kenako Davide mfumu anaimirira ndipo anati: “Ndimvereni inu abale anga ndi anthu anga. Ineyo ndinafunitsitsa mumtima mwanga+ kumanga nyumba yoti likasa la pangano la Yehova lizikhalamo, ndiponso yoti ikhale monga chopondapo mapazi+ cha Mulungu wathu, ndipo ndinakonzekera kuimanga.+
7 Koma ine ndidzalowa m’nyumba yanu+Chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndidzawerama nditayang’ana kumene kuli kachisi wanu wopatulika chifukwa chokuopani.+
2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.