Salimo 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ Salimo 84:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Inu Yehova wa makamu,+Ine ndimakondadi chihema chanu chachikulu!+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+