Mateyu 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo. Chivumbulutso 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzombelo lili ndi mfumu. Mfumuyo ndiye mngelo wa phompho.+ M’Chiheberi, dzina lake ndi Abadoni, koma m’Chigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.+
39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo.
11 Dzombelo lili ndi mfumu. Mfumuyo ndiye mngelo wa phompho.+ M’Chiheberi, dzina lake ndi Abadoni, koma m’Chigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.+